Zimene Achinyamata Anzanu Amanena
Nkhanza Zokhudza Kugonana
Vidiyoyi ikusonyeza achinyamata 5 amene akufotokoza tanthauzo la nkhanza zokhudza kugonana ndiponso chifukwa chake sitiyenera kuona nkhaniyi mopepuka.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndizitani Ngati Ena Akundichitira Zachipongwe?
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe tanthauzo la kuchitiridwa zachipongwe komanso zimene mungachite ngati mutachitiridwa zachipongwezo.
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Ndingatani Kuti Anthu Ena Asamandichitire Zachipongwe?
Mfundo 7 zogwirizana ndi zimene Baibulo limanena, zingakuthandizeni kupirira anthu ena akamakuchitirani zachipongwe kapena kukukamizani kuti mugone nawo.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Nkhanza za Kugonana?—Gawo 1: Mmene Mungadzitetezere
Pali njira zitatu zimene zingakuthandizeni kuti mupewe kuchitidwa nkhanza zokhudza kugonana.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Kukopana Kuli Ndi Vuto?
Kodi kukopana n’kutani? N’chifukwa chiyani anthu ena amakopana? Kodi kukopana kuli ndi vuto?
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana?
Ngati mutafunsidwa kuti: ‘Kodi sunagonanepo ndi munthu chibadwire?’ kodi mungathe kugwiritsa ntchito Baibulo poyankha?
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula?
Kodi munthu wina amakukakamizani kuti mumutumizire zolaula? Kodi kutumizirana zolaula kuli ndi mavuto otani? Kodi ndi kukopana basi?
ZIMENE ACHINYAMATA ANZANU AMANENA