Uthenga Wabwino Wolembedwa ndi Mateyo
Macaputala
Za m'Bukuli
-
-
ULALIKI WA PA PHILI (1-48)
-
Yesu ayamba kuphunzitsa pa phili (1, 2)
-
Zinthu 9 zopangitsa anthu kukhala acimwemwe (3-12)
-
Mcele ndi nyale (13-16)
-
Yesu anabwela kudzakwanilitsa Cilamulo (17-20)
-
Uphungu pa nkhani ya mkwiyo (21-26), cigololo (27-30), kusudzulana (31, 32), malumbilo (33-37), kubwezela (38-42), kukonda adani athu (43-48)
-
-
-
-
Yesu ndiye “Mbuye wa Sabata” (1-8)
-
Munthu wa dzanja lopuwala acilitsidwa (9-14)
-
Mtumiki wa Mulungu wokondedwa (15-21)
-
Yesu atulutsa ziwanda mwa mphamvu ya mzimu woyela (22-30)
-
Chimo limene silingakhululukidwe (31, 32)
-
Mtengo umadziwika ndi zipatso zake (33-37)
-
Cizindikilo ca Yona (38-42)
-
Mzimu wonyansa ukabwelela mwa munthu (43-45)
-
Amai a Yesu ndi abale ake (46-50)
-
-
-
MAFANIZO ONENA ZA UFUMU (1-52)
-
Wofesa mbeu (1-9)
-
Cifukwa cake Yesu anali kusewenzetsa mafanizo (10-17)
-
Kufotokoza tanthauzo la wofesa mbeu (18-23)
-
Tiligu ndi namsongole (24-30)
-
Kanjele ka mpilu ndi zofufumitsa (31-33)
-
Kusewenzetsa mafanizo kunakwanilitsa ulosi (34, 35)
-
Kufotokoza tanthauzo la tiligu ndi namsongole (36-43)
-
Cuma cobisika ndi ngale yamtengo wapatali (44-46)
-
Khoka (47-50)
-
Cuma catsopano komanso cakale (51, 52)
-
-
Yesu akanidwa kwao (53-58)
-
-
-
Ansembe akonza ciwembu cakuti aphe Yesu (1-5)
-
Yesu athilidwa mafuta onunkhila (6-13)
-
Pasika wothela komanso kupelekedwa kwa Yesu (14-25)
-
Kukhazikitsidwa kwa Mgonelo wa Ambuye (26-30)
-
Yesu akambilatu kuti Petulo adzamukana (31-35)
-
Yesu apemphela m’munda wa Getsemani (36-46)
-
Yesu agwidwa (47-56)
-
Yesu azengedwa mlandu m’Khoti Yaikulu ya Ayuda (57-68)
-
Petulo akana Yesu (69-75)
-

