A7-C
Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu Umene Yesu Anacita mu Galileya (Mbali 1)
|
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYO |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
|---|---|---|---|---|---|---|
|
30 |
Galileya |
Yesu alengeza koyamba kuti “Ufumu wa Kumwamba wayandikila” |
||||
|
Kana; Nazareti; Kaperenao |
Acilitsa mnyamata; awelenga mpukutu wa Yesaya; apita ku Kaperenao |
|||||
|
Nyanja ya Galileya, pafupi ndi Kaperenao |
Aitana ophunzila anai: Simoni ndi Andireya, Yakobo ndi Yohane |
|||||
|
Kaperenao |
Acilitsa apongozi aakazi a Simoni ndi ena |
|||||
|
Galileya |
Ulendo woyamba mu Galileya ali ndi ophunzila anai |
|||||
|
Acilitsa wakhate; khamu limutsatila |
||||||
|
Kaperenao |
Acilitsa munthu wofa ziwalo |
|||||
|
Aitana Mateyo; akudya ndi okhometsa msonkho; amufunsa za kusala kudya |
||||||
|
Yudeya |
Alalikila m’sunagoge |
|||||
|
31, Pasika |
Yerusalemu |
Acilitsa mwamuna wodwala ku Beti-zama; Ayuda afuna kumupha |
||||
|
Abwelela kucokela ku Yerusalemu (?) |
Ophunzila abudula ngala pa Sabata; Yesu “ndiye Mbuye wa Sabata” |
|||||
|
Galileya; Nyanja ya Galileya |
Acilitsa dzanja la mwamuna wina pa Sabata; khamu limutsatila; acilitsanso anthu ambili |
|||||
|
Phili la kufupi ndi ku Kaperenao |
Asankha atumwi 12 |
|||||
|
Kufupi ndi ku Kaperenao |
Ulaliki wapaphili |
|||||
|
Kaperenao |
Acilitsa wanchito wa kapitawo wa asilikali |
|||||
|
Naini |
Aukitsa mwana wa mkazi wamasiye |
|||||
|
Tiberiyo; Galileya (Naini kapena kufupi) |
Yohane atumiza ophunzila ake kwa Yesu; coonadi ciululidwa kwa ana; joko yake ndi yosabvuta kunyamula |
|||||
|
Galileya (Naini kapena kufupi) |
Mai wocimwa athila mafuta mapazi ake; fanizo la nkhongole |
|||||
|
Galileya |
Ulendo waciwili wokalalikila ndipo ali limodzi ndi atumwi 12 |
|||||
|
Atulutsa ziwanda; chimo losakhululukidwa |
||||||
|
Akana kupeleka cizindikilo cake, koma apeleka cizindikilo ca Yona |
||||||
|
Mai ake ndi abale ake abwela kudzamuona; akamba kuti ophunzila ake ndio abale ake |

