B14-B
Ndalama ndi Kulemela kwa Zinthu
Ndalama ndi Kulemela kwa Zinthu m’Malemba a Ciheberi
Gera (1⁄20 ya sekeli)
Magalamu 0.57
Magera 10 = Beka imodzi
Beka
Magalamu 5.7
Mabeka awili = Sekeli imodzi
Pimu
Magalamu 7.8
Pimu imodzi = 2⁄3 ya sekeli
Kulemela kwa sekeli
Sekeli
Magalamu 11.4
Masekeli 50 = Mina imodzi
Mina
Magalamu 570
Mamina 60 = Talente imodzi
Talente
Makilogilamu 34.2
Dariki
(ya ku Perisiya, yagolide)
Magalamu 8.4
Ezara 8:27
Ndalama ndi Kulemela kwa Zinthu m’Malemba a Cigiriki
Dinari
(ya Aroma, yasiliva)
Makwadiransi 64
Magalamu 3.85
= Malipilo a Tsiku Limodzi (Maola 12)
Didirakima
(ya Agiriki, yasiliva)
Madirakima awili
Magalamu 6.8
= Malipilo a Masiku Awili
Tetiradirakima ya ku Antiokeya
Tetiradirakima ya ku Turo (Sekeli ya siliva ya ku Tulo)
Tetiradirakima
(ya Agiriki, yasiliva; imachedwanso siteta yasiliva)
Madirakima anai
Magalamu 13.6
= Malipilo a Masiku Anai
Talente
Mamina 60
Makilogilamu 20.4
= Malipilo a zaka pafupifupi 20

