Kukhulupilila Mulungu
Cikhulupililo n’camphamvu kwambili ndipo cimathandiza munthu kukhala na mtendele wa mumtima pali pano, komanso ciyembekezo codalilika ca m’tsogolo. Ngati simunakhulupililepo Mulungu, munaleka kumukhulupilila, kapenanso mufuna kulimbitsa cikhulupililo canu, Baibo ingakuthandizeni.

