Umoyo ndi Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano
Kabuku ka Misonkhano ya Umoyo ndi Utumiki Wathu Wacikhristu, kamaonetsa ndandanda ndi nkhani zophunzila pa msonkhano wa Mboni za Yehova wa mkati mwa mlungu, kuphatikizapo mbali ya kuwelenga Baibo kwa mlungu ndi mlungu. Msonkhanowu ndi waulele ndipo aliyense angapezekepo.

