CIMASULILO CA DZIKO LATSOPANO

Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Cinyanja
Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
/assets/ct/e5be1b2cc6/images/syn_placeholder_sqr.png
nwt

Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Inamasulidwa kucokela ku Baibo ya Cingelezi ya NEW WORLD TRANSLATION OF THE HOLY SCRIPTURES

—Yokonzedwanso mu 2013—

“Yehova, [יהוה, YHWH] Ambuye Wamkulukulu, akunena kuti: ‘. . . Taonani! Nikulenga kumwamba kwatsopano na dziko lapansi latsopano. Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukika kapena kuvutitsa mtima wa munthu.’”Yesaya 65:13, 17, nwt-E; onaninso 2 Petulo 3:13.

 
 

Baibo imeneyi, yathunthu kapena mbali yake, ikupezeka m’zinenelo zoposa 270. Kuti muone zinenelo zonse, pitani pa www.jw.org.

Mabaibo Onse a Cimasulilo ca Dziko Latsopano Amene Apulintidwa Alipo Pafupifupi:

250,000,000

Yocitidwa Apudeti mu August 2025

Baibo ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi.

Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano

New World Translation of the Holy Scriptures

Cinyanja (nwt-CIN)

Made in Japan

4-7-1 Nakashinden ,

Ebina City, Kanagawa-Pref,

243-0496 Japan