Sayansi na Baibo
Kodi Baibo imagwilizana na zimene asayansi amaphunzitsa? Kodi Baibo imakamba zoona pankhani ya sayansi? Ŵelengani zimene asayansi amanena komanso zimene cilengedwe cimaonetsa pankhani imeneyi.
Zimene Anthu Amakamba Ponena za Mmene Moyo Unayambila
Umboni Wasayansi Woonetsa Kuti Baibo ni Lolondola
Mabuku
Zodabwitsa za Cilengedwe Zimaonetsa Ulemelelo wa Mulungu
Ngati tayang’anitsitsa cilengedwe cotizungulila, tingaone makhalidwe a Mlengi, ndipo tingamuyandikile.

