Kodi Zinangocitika Zokha?

Nyama za Pamtunda

Kodi luso la nchenzi la zomanga-manga linacita kulengedwa?

Onani cifukwa cake nchenzi zimachedwa akatswili a zomanga-manga m’cilengedwe.

Kayendedwe ka Magazi m’Thupi la Nyamalikiti—Kodi Zinangocitika Zokha?

Pokhala nyama yaitali pa nyama zonse za kuchile, nyamalikiti imakumana ndi bvuto la kulimbana ndi kuthamanga kwambili kwa magazi. Kodi imacita bwanji zimenezi?