ZIMENE BAIBO IMAPHUNZITSA

Mbili Yakale komanso Baibo

Cinyanja
Mbili Yakale komanso Baibo
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1011569/univ/art/1011569_univ_sqr_xl.jpg

Mbili Yakale komanso Baibo

Baibo ni buku lapadela kwambili tikaganizila zimene zinacitika kuti isungidwe kwa nthawi yaitali, imasulilidwe komanso kufalitsidwa. Zimene akatswili apeza posacedwapa zikupitilizabe kutsimikizila kuti ni yolondola. Kaya muli m’cipembedzo canji, nanunso mungavomeleze kuti Baibo siingalingane na buku ina iliyonse.