Nyuzi
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tikambilana za kusintha kwa kamvedwe kathu pa nkhani yazigao zikulu-zikulu za magazi. Vidiyoyi, komanso nkhani yogwilizana nayo yakuti “Mafunso Ocokela kwa Owelenga” pamodzi ndi chati, zatulutsidwa tsopano mu Cinyanja. Vidiyoyi, chati komanso nkhani yake zidzapezeka m’zinenelo zina posacedwapa.
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tikambilana za kusintha kwa kamvedwe kathu pa nkhani yazigao zikulu-zikulu za magazi. Vidiyoyi, komanso nkhani yogwilizana nayo yakuti “Mafunso Ocokela kwa Owelenga” pamodzi ndi chati, zatulutsidwa tsopano mu Cinyanja. Vidiyoyi, chati komanso nkhani yake zidzapezeka m’zinenelo zina posacedwapa.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tikambilana cifukwa cake tiyenela kudya cakudya cauzimu tsiku ndi tsiku. Tikambilananso zinthu zatsopano zimene tingauzeko ena mu ulaliki.
Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tifotokoza malipoti olimbikitsa a posacedwa, okhudza maulendo aubusa komanso maulendo a oimila likulu amene amacitika ku maofesi a nthambi. Tifotokozanso zocitika zokhudza ufulu wathu wa kulambila ku Norway ndi ku Sweden.
Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tikambilana za kupilila kwa abale ndi alongo athu ku Russia kucokela pamene nchito yathu inaletsedwa m’dzikolo, zaka 9 zapitazo. Cina, tilengeza za kutulutsidwa kwa Magao 4, 5, ndi 6 a vidiyo yakuti, Mbili ya Umoyo wa Yesu.
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tidzafotokoza kamvedwe katsopano kokhudza mmene wodwala angaseŵenzetsele magazi ake pa nkhani zokhudza cithandizo ca cipatala.
Ciunikilo Na. 1 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tikambilana malangizo atsopano a motsogozela maphunzilo a Baibo mogwila mtima pogwilitsila nchito buku lakuti, Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tione mmene mavidiyo a sewelo yakuti, Mbili ya Umoyo wa Yesu akukhudzila abale ndi alongo athu.
Ciunikilo Na. 7 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tione zocitika zosangalatsa za mu Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2025. Tionanso mmene Yehova akudalitsila nchito yathu yolalikila pa dziko lonse.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino tikambilane zokhudza lemba la caka ca 2026 komanso nyimbo yatsopano.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tikambilana mfundo zimene zingatithandize kupanga zisankho zanzelu pa nkhani yoonjezela maphunzilo a kuthupi.

