NKHANI ZATSOPANO

“Musaope”

Cinyanja
“Musaope”
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/702026082/univ/art/702026082_univ_sqr_xl.jpg

JULY 6, 2026
RUSSIA

Mlongo Irina Shishkina

“Musaope”

“Musaope”

Pa June 29, 2026, Khoti la Boma la Rudnichniy ku Prokopyevsk linapeza Mlongo Irina Shishkina ndi mlandu ndipo linamulamula kucita ukaidi wosapita ku ndende wa zaka 4. Pali pano iye safunikila kupita ku ndende.

Mbili Yake

Tili ndi cikhulupililo conse kuti Yehova adzapitiliza kuthandiza ndi kulimbikitsa anthu ake, pamene tikupilila mokhulupilika mabvuto m’masiku otsiliza ano.—Ekisodo 14:13.