Onani zimene zilipo

Kuyankha Mafunso a m’Baibo

Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni. Sankhani funso imene mungakonde pa mbali zili pansipa.

Phunzilani Baibo

N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo?

Anthu mamiliyoni akupedza mayankho a mafunso awo ofunika kwambili m’Baibo. Kodi mungafune kukhala m’modzi wa iwo?

Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji?

Zungulile dziko lonse, Mboni za Yehova zimadziŵika cifukwa ca pulogilamu yawo yophunzitsa Baibo kwaulele. Onani mmene imacitikila.

Pemphani kuti wa Mboni adzakucezeleni

Kambilanani nkhani ya m’Baibo na Mboni za Yehova, kapena laŵani maphunzilo a Baibo amene timapeleka.