Baibo

Gwelo Lake na Kudalilika Kwake

Kodi Baibo Anaisintha Kapena Anangoisinthako Zina?

Popeza kuti Baibo ni buku lakale kwambili, kodi tingatsimikize bwanji kuti uthenga umene ulimo wakhala ukutetezedwa kuti ukhale wolondola?

Kodi Sayansi Imagwilizana na Baibo?

Kodi Baibo ili na mfundo zolakwika zokhudza sayansi?

Mapeto a Dziko

Kodi Nkhondo ya Aramagedo N’ciyani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibo. Koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imachulidwa m’Baibo lonse.

Anthu, Malo, na Zinthu

Kodi Mulungu Anaseŵenzetsa Cisanduliko Polenga Zamoyo Zosiyanasiyana?

Palibe mfundo iliyonse m’Baibo imene imatsutsana na asayansi amene amati zolengedwa zamoyo zimasintha malinga na mtundu wake.

Mmene Imatithandizila

Kodi Ndalama N’zimene Zimabweletsa Mavuto Onse?

Zimene anthu ambili amakonda kukamba zakuti “ndalama ndiye muzu wa zoipa zonse” zimangoonetsa kuti samvetsa zimene Baibo imakamba.

Kodi Baibo Ingathandize Anthu Odwala Matenda Osathelapo?

Inde! Dziŵani njila zitatu zimene zingakuthandizeni ngati muli na matenda osathelapo.