N’ciani Catsopano?
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
Adzauka
Munthu amene timakonda akamwalila, ciyembekezo cathu cakuti akufa adzauka cimatilimbikitsa.
UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO
January–February 2027
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
Ndimakudalilani
Yehova ndi thanthwe langa, cishango canga, ndipo tiyenela kudzipeleka kwa iye ndi kumudalila ndi mtima wonse.
MABULOSHA NDI TUMABUKU
Examining the Scriptures Daily—2027
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
‘Muposa mpheta zambili’
Simungathe kuona kufunika kwanu, koma Yehova amaona. Nyimbo iyi itikumbutsa kuti ngakhale panthawi pamene tiona kuti ndife osafunika, Yehova komanso atumiki ake amene amamukonda, amatikonda kwambili.
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
Ndi Cikhulupililo
Panthawi ya cipolowe komanso mabvuto azacuma, banja lina linaona cikondi ca Yehova, iye anawalimbikitsa, kuwapatsa ciyembekezo, ndipo analimbitsa cikhulupililo cao.
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Mphatso Imene Yehova Wapeleka kwa Amene Ali ndi Bvuto Losamva
Onani cifukwa cake tsopano timatha kumasulila Mabaibo ambili a cinenelo camanja kuposa n’kale lonse.
MAFUNSO OCOKELA KWA OWELENGA
Kodi Mboni za Yehova Zimaonetsa Bwanji Kuti Zimalemekeza Moyo?
Dziwani mmene Mboni za Yehova zimaonetsela kuti zimalemekezela moyo.
CHATI
Zigao Zocokela ku Magazi Athunthu
Chati imeneyi ionetsa zigao zocokela ku magazi athunthu ndipo ingakuthandizeni kupanga zisankho zokhudza kulandila cithandizo ca mankhwala cofuna kugwilitsila nchito magazi.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Kodi Mukukumbukila?—December 2026
Kodi munawelenga mosamala magazini a Nsanja ya Mlonda a caka cino? Onani zimene mungakumbukile.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Mapindu Opatula Nthawi Yokhala Patokha
Onani zimene Yesu anacita kuti apeze nthawi yokhala kwayekha, komanso cifukwa cake tifunika kutengela citsanzo cake.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Mfundo Zitatu Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipeleka Mapemphelo Otalikilapo
Kodi mungatani kuti muzipemphela kwa nthawi yaitali, kuti mufotokoze maganizo anu ndi kukhutula zonse za mumtima mwanu kwa Mulungu?
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Mau a m’Baibo—“Ngati N’kotheka Yesetsani, . . . Kukhala Mwamtendele Ndi Anthu Onse”
Akhristu oona amayesetsa kukhala mwamtendele ndi anthu onse. Koma nthawi zina kucita zimenezi kungakhale kobvuta. Cifukwa ciani?
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
December 2026
Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila kuyambila February 1-28, 2027.

