Pulogilamu ya Msonkhano Wadela wa 2026-2027 Wokhala ndi Woyang’anila Dela
“Wosangalala ndi Munthu Amene Amadalila Yehova”
Pulogilamu ya cigao ca m’maŵa komanso ca masana ca msonkhano wadela wokhala ndi woyang’anila dela.
Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
Mafunsowa adzayankhidwa pa msonkhano uno.

