Mtendele Komanso Cimwemwe
Tikakumana na mavuto aakulu tingayambe kuganiza kuti n’zosatheka kukhala acimwemwe komanso kukhala na mtendele wa mumtima. Koma Baibo yathandiza anthu ambili kupilila mavuto omwe amakumana nawo tsiku na tsiku. Yaŵathandizanso kucepetsako nkhawa komanso kuthana na mavuto ena ndipo yaŵathandiza kuona kuti moyo uli na colinga. Inunso Baibo ingakuthandizeni kuti muzikondwela.
Umoyo Wathanzi
Nchito Komanso Ndalama
Ubwenzi
Zizolowezi Komanso Makhalidwe Oipa
N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe
Cikwati canu ndi banja lanu lingakhale lacimwemwe ngati mutsatila mfundo za m’Baibulo.
Phunzilani Baibo
N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo?
Anthu mamiliyoni akupedza mayankho a mafunso awo ofunika kwambili m’Baibo. Kodi mungafune kukhala m’modzi wa iwo?
Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji?
Zungulile dziko lonse, Mboni za Yehova zimadziŵika cifukwa ca pulogilamu yawo yophunzitsa Baibo kwaulele. Onani mmene imacitikila.
Pemphani kuti wa Mboni adzakucezeleni
Kambilanani nkhani ya m’Baibo na Mboni za Yehova, kapena laŵani maphunzilo a Baibo amene timapeleka.

