Pulogilamu ya Msonkhano Wadela wa 2026-2027 Wokhala ndi Woimila Nthambi
‘Sangalalani Cifukwa ca Yehova’
Pulogilamu ya cigao ca m’maŵa komanso ca masana ca msonkhano wadela wokhala ndi woimila nthambi.
Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
Mafunsowa adzayankhidwa pa msonkhano uno.

