Baibo Imakamba Zinthu Zakale Molondola
Malo Ochulidwa m'Baibo
Kugwa kwa Nineve
Pamene ulamulilo wa Asuri unakhala wamphamvu kwambili, mneneli wa Mulungu analosela cinthu cimene anthu sanayembekezele.
KODI MUDZIŴA?—July 2015
Baibulo limafotokoza kuti madela ena a Dziko Lolonjezedwa anali ndi nkhalango zoŵilila. Popeza kuti masiku ano kulibe nkhalango zoŵilila ngati za m’nthawi ya Isiraeli, kodi zimene Baibulo limanena n’zoona?
Anthu a m'Baibo
Kodi Mudziŵa?—March 2020
Kuwonjezela pa zimene Baibo imakamba, kodi palinso umboni wotani woonetsa kuti Aisiraeli anakhalako akapolo ku Iguputo?
Dzina la m’Baibo pa Mtsuko Wakale
Mapale a mtsuko wakale umene unaumbidwa zaka 3,000 zapitazo anacititsa cidwi akatswili ocita kafuku-fuku. Mapalewo anawapeza mu 2012. N’ciani maka-maka cimene cinawacititsa cidwi?
Kodi Mudziŵa?—February 2020
Kodi zofukula za m’matongwe zimaonetsa bwanji kuti Belisazara wa ku Babulo anali mfumu?
Umboni Winanso wa Zinthu Zakale
Mwina simungadziŵe kuti Tatenai anali ndani, koma umboni wa zinthu zakale utsimikizila za munthu ameneyu.
Zocitika za m'Baibo
Kodi Mudziŵa?—June 2022
Kodi Aroma anali kulola munthu wopacikidwa pa mtengo, monga Yesu, kuti mtembo wake uikidwe m’manda?
Umoyo wa Anthu M'nthawi za m'Baibo
Ndi zinthu ziti zimene zinali kucitika pa mageti a mzinda ochulidwa m’Baibo?
Ndi zinthu ziti zimene zinali kucitika pa mageti a mzinda ochulidwa m’Baibo?
Nyimbo m’nthawi ya Aisiraeli akale
Kodi nyimbo zinali zofunika motani kwa Aisiraeli akale?
Mtundu wa Galeta Limene Nduna ya ku Itopiya Inakwela
Ni galeta la mtundu wanji limene nduna ya ku Itiyopiya inakwela pamene Filipo anakamba nayo?
Kaumbidwe ka nchelwa kakale, kaonetsa kuti Baibo ni yolondola
Kodi nchelwa zimene anapeza pa matongwe a Babulo wakale komanso mmene anaziumbila, zionetsa bwanji kuti Baibo ni yolondola?
Kodi Mudziŵa?—June 2022
Kodi anthu ochulidwa m’Baibo anali kudziŵa bwanji poyambila caka kapena mwezi?
Kodi Mudziŵa?—October 2017
Kodi Ayuda anali na cizoloŵezi canji cimene cinapangitsa Yesu kuwaletsa kulumbila?
Kodi Mudziŵa?—Nsanja ya Mlonda Na. 5 2017
Kodi Yesu ananyoza pamene anacha anthu osakhala Ayuda kuti “tiagalu”?
Kodi Mudziŵa? —June 2017
N’cifukwa ciani Yesu anakamba kuti amalonda amene anali kugulitsa ziweto m’kacisi anali “acifwamba”?
Kodi Mudziŵa?—October 2016
M’nthawi ya atumwi, ni ufulu wabwanji umene Aroma anapatsa olamulila aciyuda ku Yudeya? Kodi n’zoona kuti kale munthu wina anali kubyala namsongole m’munda wa mnzake?
Kodi Mudziŵa—December 2015
Kodi Ayuda amene anapezeka pa Pentekosite mu 33 C.E. anacokeladi “mu mtundu uliwonse mwa mitundu ya pansi pa thambo”? Kodi anthu masauzande ambili amene anali kubwela ku Yerusalemu kudzacita zikondwelelo zaciyuda anali kugona kuti?

