Cinyanja
Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Ciyambi ca Utumiki wa Yesu
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt masa. 550-551

A7-B

Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Ciyambi ca Utumiki wa Yesu

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYO

MALIKO

LUKA

YOHANE

29, cakumapeto kwa caka

Mtsinje wa Yorodano, kapena kufupi ndi Betaniya wa kutsidya kwa Yorodano

Ubatizo ndi kudzozedwa kwa Yesu; Yehova amulengeza kuti ndi Mwana wake komanso kuti amakondwela naye

3:13-17

1:9-11

3:21-38

 

Cipululu ca Yudeya

Ayesedwa ndi Mdyelekezi

4:1-11

1:12, 13

4:1-13

 

Betaniya wa kutsidya lina la Yorodano

Yohane M’batizi akamba kuti Yesu ndi Mwanawankhosa wa Mulungu; ophunzila oyambilila atsatila Yesu

     

1:15, 19-51

Kana wa ku Galileya; Kaperenao

Cozizwitsa coyamba, asandutsa madzi kukhala vinyo; apita ku Kaperenao

     

2:1-12

30, Pasika

Yerusalemu

Ayeletsa kacisi

     

2:13-25

Akambilana ndi Nikodemo

     

3:1-21

Yudeya; Ainoni

Apita kumidzi ya ku Yudeya, ophunzila ake abatiza anthu; umboni womaliza wa Yohane wokhudza Yesu

     

3:22-36

Tiberiyo; Yudeya

Yohane aikidwa m’ndende; Yesu acoka apita ku Galileya

4:12; 14:3-5

6:17-20

3:19, 20

4:1-3

Sukari, ku Samariya

Pa ulendo wa ku Galileya, aphunzitsa Asamariya

     

4:4-43

Cipululu ca Yudeya