Cinyanja
Kodi Baibo Imakamba Zolondola pa Nkhani za Sayansi?
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt tsa. 11

FUNSO 4

Kodi Baibo Imakamba Zolondola pa Nkhani za Sayansi?

“Iye anatambasula thambo lakumpoto pamwamba pa malo opanda kanthu, ndipo dziko lapansi analiika mʼmalele.”

Yobu 26:7

“Mitsinje yonse imakathila mʼnyanja koma nyanjayo sidzaza. Imabwelela kumalo kumene ikucokela kuti ikayambilenso kuyenda.”

Mlaliki 1:7

“Pali winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi lomwe ndi lozungulila.”

Yesaya 40:22