B12
Wiki Yomaliza ya Yesu Padziko Lapansi (Mbali 1)
Yerusalemu ndi Madela Ozungulila
-
Kacisi
-
Munda wa Getsemani (?)
-
Nyumba ya Bwanamkubwa
-
Nyumba ya Kayafa (?)
-
Nyumba ya Herode Antipa (?)
-
Dziwe la Betesida
-
Dziwe la Siloamu
-
Holo ya Sanihedirini (?)
-
Gologota (?)
-
Munda wa Magazi (?)
Zocitika za pa: Nisani 8 | Nisani 9 | Nisani 10 | Nisani 11
Nisani 8 (Sabata)
DZUWA LITALOWA (Masiku a Ayuda anali kuyamba ndi kutha dzuwa likalowa)
-
Afika ku Betaniya kutatsala masiku 6 kuti Pasika acitike
M’MAWA
DZUWA LITALOWA
Nisani 9
DZUWA LITALOWA
-
Akudya ndi Simoni wakhate
-
Mariya adzoza Yesu ndi nado
-
Ayuda apita kukaona Yesu komanso Lazaro
M’MAWA
-
Alowa mu Yerusalemu mwaulemelelo
-
Aphunzitsa m’kacisi
DZUWA LITALOWA
Nisani 10
DZUWA LITALOWA
-
Agona ku Betaniya
M’MAWA
-
Alawilila kupita ku Yerusalemu
-
Ayeletsa kacisi
-
Yehova alankhula kucokela kumwamba
DZUWA LITALOWA
Nisani 11
DZUWA LITALOWA
M’MAWA
-
Asewenzetsa mafanizo pophunzitsa m’kacisi
-
Adzudzula Afarisi
-
Aona pamene mkazi wamasiye akucita copeleka
-
Ali pa Phili la Maolivi ndipo akambilatu za kuonongedwa kwa Yerusalemu, komanso apeleka cizindikilo ca kukhalapo kwake

