A7-D
Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu Umene Yesu Anacita mu Galileya (Mbali 2)
|
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYO |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
|---|---|---|---|---|---|---|
|
31 kapena 32 |
Dela la Kaperenao |
Yesu afotokoza mafanizo a Ufumu |
||||
|
Nyanja ya Galileya |
Akhalitsa bata namondwe pomwe ali m’bwato |
|||||
|
Dela la Dadara |
Atumiza ziwanda m’nkhumba |
|||||
|
Mwina ku Kaperenao |
Acilitsa mzimai amene anali ndi matenda otaya magazi; aukitsa mwana wamkazi wa Yairo |
|||||
|
Kaperenao (?) |
Acilitsa munthu wakhungu komanso munthu wosalankhula |
|||||
|
Nazareti |
Akanidwanso mumzinda wakwao |
|||||
|
Galileya |
Ulendo wacitatu wa ku Galileya; atumiza atumwi kukalalikila |
|||||
|
Tiberiyo |
Herode adula mutu Yohane M’batizi; Herode athedwa nzelu atamva za Yesu |
|||||
|
32, Pasika atayandikila (Yoh 6:4) |
Kaperenao (?); Kumpoto cakum’mawa kwa Nyanja ya Galileya |
Atumwi abwelako kokalalikila; Yesu adyetsa amuna 5,000 |
||||
|
Kumpoto cakum’mawa kwa Nyanja ya Galileya; Genesareti |
Ayesa kulonga Yesu ufumu; ayenda pamadzi; acilitsa anthu ambili |
|||||
|
Kaperenao |
Yesu akamba kuti iye ndi “cakudya copatsa moyo”; ambili asiya kumutsatila |
|||||
|
32, Pambuyo pa Pasika |
Mwina ku Kaperenao |
Awadzudzula cifukwa ca miyambo |
||||
|
Foinike; Dekapole |
Acilitsa mwana wamkazi wa mai wacisirofoinike; adyetsa amuna 4,000 |
|||||
|
Magadani |
Apeleka cizindikilo ca Yona |

