A7-H
Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu mu Yerusalemu (Mbali 2)
|
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYO |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
|---|---|---|---|---|---|---|
|
Nisani 14 |
Yerusalemu |
Yesu aulula kuti Yudasi ndiye adzam’peleka ndipo amuuza kuti acoke |
||||
|
Ayambitsa Mgonelo wa Ambuye (1Ak 11:23-25) |
||||||
|
Anenelatu kuti Petulo adzam’kana komanso kuti atumwi adzabalalika |
||||||
|
Alonjeza kuti adzawapatsa mthandizi; fanizo la mpesa; lamulo lakutitizikondana; apemphela kothela ndi atumwi ake |
||||||
|
Getsemani |
Yesu abvutika maganizo; apelekedwa ndi kumangidwa |
|||||
|
Yerusalemu |
Afunsidwa mafunso ndi Anasi; azengedwa mlandu ndi Kayafa komanso Khoti Yaikulu ya Ayuda; Petulo amukana |
|||||
|
Yudasi amene anam’peleka uja adzimangilila (Mac 1:18, 19) |
||||||
|
Aonekela pamaso pa Pilato, kenako kwa Herode n’kubwelelanso kwa Pilato |
||||||
|
Pilato ayesetsa kuti amumasule koma Ayuda asankha Baraba; aweluzidwa kuti aphedwe mwa kumukhomelela pamtengo |
||||||
|
(ca m’ma 3 koloko masana, Lacisanu) |
Gologota |
Akufa pa mtengo wozunzikilapo |
||||
|
Yerusalemu |
Atsitsa mtembo wake pa mtengo ndi kukauika m’manda |
|||||
|
Nisani 15 |
Yerusalemu |
Ansembe ndi Afarisi aika alonda pa manda n’kutsekapo |
||||
|
Nisani 16 |
Yerusalemu ndi madela apafupi; Emau |
Yesu aukitsidwa; aonekela kasanu kwa ophunzila ake |
||||
|
Pambuyo pa Nisani 16 |
Yerusalemu; Galileya |
Aonekelanso kwa ophunzila ake kangapo (1Ak 15:5-7; Mac 1:3-8); aphunzitsa; alamula ophunzila kuti akaphunzitse anthu kukhala ophunzila ake |
||||
|
Iyari 25 |
Phili la Maolivi, pafupi ndi Betaniya |
Yesu akwela kumwamba pambuyo pa masiku 40 ataukitsidwa (Mac 1:9-12) |

