Cinyanja
Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Utumiki wa Yesu mu Galileya (Mbali 3) Komanso mu Yudeya
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt masa. 556-557

A7-E

Zocitika Zikulu-zikulu mu Umoyo wa Yesu Ali Padziko Lapansi—Utumiki wa Yesu mu Galileya (Mbali 3) Komanso mu Yudeya

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYO

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, pambuyo pa Pasika

Nyanja ya Galileya; Betsaida

Akwela bwato kupita ku Betsaida, Yesu awacenjeza za cofufumitsa ca Afarisi; acilitsa munthu wakhungu

16:5-12

8:13-26

   

Kaisareya wa ku Filipi

Makiyi a Ufumu; akambilatu za imfa yake ndi kuukitsidwa

16:13-28

8:27–9:1

9:18-27

 

Mwina pa Phili la Herimoni

Kusandulika; Yehova alankhula

17:1-13

9:2-13

9:28-36

 

Kaisareya wa ku Filipi

Acilitsa mnyamata wogwidwa ndi ciwanda

17:14-20

9:14-29

9:37-43

 

Galileya

Akambilatunso za imfa yake

17:22, 23

9:30-32

9:43-45

 

Kaperenao

Akhoma msonkho ndi ndalama imene apeza mkamwa mwa nsomba

17:24-27

     

Amene ali wamkulu kwambili mu Ufumu; fanizo la nkhosa yosocela komanso la kapolo wosakhululuka

18:1-35

9:33-50

9:46-50

 

Galileya-Samariya

Apita ku Yerusalemu, auza ophunzila kuika patsogolo Ufumu

8:19-22

 

9:51-62

7:2-10

Utumiki Womaliza Umene Yesu Anacita ku Yudeya

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYO

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, Cikondwelelo ca Misasa (kapena kuti ca Mahema)

Yerusalemu

Aphunzitsa pa Cikondwelelo; asilikali atumidwa kukagwila Yesu

     

7:11-52

Akamba mau akuti “Ine ndine kuwala kwa dziko”; acilitsa munthu yemwe anabadwa wakhungu

     

8:12–9:41

Mwina ku Yudeya

Atuma ophunzila 70 ndipo iwo abwelako ali acimwemwe

   

10:1-24

 

Yudeya; Betaniya

Fanizo la Msamariya wacifundo; apita kukaona Mariya ndi Marita kunyumba kwao

   

10:25-42

 

Mwina ku Yudeya

Pemphelo lacitsanzo; fanizo lokhudza kulimbikila ndi kupemphela

   

11:1-13

 

Atulutsa ziwanda ndi cala ca Mulungu; apelekanso cizindikilo ca Yona

   

11:14-36

 

Akudya ndi Mfarisi; adzudzula cinyengo ca Afarisi

   

11:37-54

 

Mafanizo: munthu wolemela wopanda nzelu komanso mtumiki wokhulupilika

   

12:1-59

 

Acilitsa mzimai wopindika msana pa Sabata; fanizo la kanjele ka mpilu komanso la zofufumitsa

   

13:1-21

 

32, Cikondwelelo Copeleka Kacisi kwa Mulungu

Yerusalemu

Fanizo la m’busa wabwino; Ayuda afuna kumuponya miyala; acoka ndipo apita ku Betaniya wa kutsidya la Yorodano

     

10:1-39