Pitani ku nkhani yake

Baibulo

Umboni Woti Nkhani za M'Baibulo ndi Zolondola

Kodi Baibulo N’chiyani?

Yambani kufufuza za uthenga wochititsa chidwi wotchedwa mawu a Mulungu.

Kodi Nkhani Zimene Zili M’Baibulo Ndi Nzeru za Anthu?

Taonani mfundo yochititsa chidwi iyi imene ili m’Baibulo.

Kodi Baibulo Ndi Lochokera kwa Mulungu?

Anthu ambiri amene analemba Baibulo amati analemba maganizo a Mulungu. N’chifukwa chiyani amatero?

Kodi Mose Ndi Amene Analemba Baibulo?

Mose analemba nawo Baibulo? Kodi ndi anthu angati amene analemba Baibulo?

Kodi Pali Munthu Amene Angadziwe Amene Analembadi Baibulo?

Anthu amene analemba Baibulo amati anauziridwa ndi Mulungu. Kodi tiyenera kukhulupirira zimene anthuwo analemba?

Kodi Baibulo Linasinthidwa Kapena Kusokonezedwa?

Popeza kuti Baibulo ndi buku lakalekale, kodi tingatsimikize bwanji kuti uthenga wake ndi wolondola mpaka pano?

Kodi Mulungu Anayamba Liti Kulenga Zinthu?

Yankho lake lagona pa mmene mawu akuti “pachiyambi” ndiponso “tsiku” anawagwiritsira ntchito m’buku la Genesis.

Kodi Sayansi Imagwirizana ndi Baibulo?

Kodi m’Baibulo muli mfundo zolakwika zokhudza sayansi?

Kodi Baibulo Ndi Buku la Azungu?

Kodi anthu amene analemba Baibulo anabadwira kuti, ndipo kwawo kunali kuti?

Kodi Nkhani Zokhudza Moyo wa Yesu Zinalembedwa Liti?

Kodi panapita nthawi yaitali bwanji kuchokera pamene Yesu anafa kufika pamene mabuku a Uthenga Wabwino analembedwa?

Kuwerenga Baibulo Komanso Kulimvetsa

N’chiyani Chingakuthandizeni Kumvetsa Baibulo?

Kaya ndife anthu otani, tikhoza kumvetsa uthenga wa Mulungu umene uli m’Malemba Opatulika.

Kodi Nkhani za M’Baibulo Zimatsutsana?

Onani nkhani zina za m’Baibulo zimene zimaoneka ngati zimatsutsana komanso mfundo zimene zingakuthandizeni kuti mumvetse nkhanizo.

Kodi Baibulo Limatanthauza Chiyani Likamanena Kuti “Mawu?”

M’Baibulo, mawu amatanthauza zinthu zingapo

Kodi Lamulo Lakuti “Diso Kulipira Diso” Limatanthauza Chiyani?

Kodi lamulo lakuti “diso kulipira diso” linkapereka ufulu woti anthu azibwezerana?

Kodi Malamulo Khumi a Mulungu Ndi Chiyani?

Kodi malamulowo anaperekedwa kwa ndani? Kodi Akhristu ayenera kuwatsatira?

Kodi Kukhala “Msamariya Wachifundo” Kumatanthauza Chiyani?

Yesu anagwiritsa ntchito nkhaniyi mwaluso pophunzitsa anthu mmene ayenera kuchitira zinthu ndi anthu ena, posatengera mtundu kapena kumene amachokera.

Kodi Tora N’chiyani?

Kodi analemba Tora ndi ndani? Kodi zimene zili mu Tora ziyenera kugwiritsidwa ntchito mpaka kalekale ndipo siziyenera kunyalanyazidwa?

Ulosi Komanso Zimene Ukuimira

Kodi Ulosi Umatanthauza Chiyani?

Kodi ulosi uliwonse wochokera kwa Mulungu umaneneratu zam’tsogolo? Ayi, osati nthawi zonse.

Kodi Manambala Otchulidwa M’Baibulo Amaimira Chiyani? Nanga Kukhulupirira Manambala N’kogwirizana ndi Mfundo za M’Baibulo?

Onani zimene manambala ena amaimira m’Baibulo, ndipo dziwani chifukwa chake zimenezi zili zosiyana ndi kukhulupirira manambala.

Kodi Ulosi wa M’Baibulo Umatiuza Zotani pa Nkhani ya Chaka cha 1914?

Ulosi wa “nthawi zokwanira 7” wopezeka mu Danieli chaputala 4 umasonyeza nthawi yapadera yokhudza ulamuliro wa anthu.

Kodi dzina la buku la m’Baibulo, lakuti Chivumbulutso, limatanthauza chiyani?

Kodi Dzina la Buku la M’Baibulo, Lakuti Chivumbulutso, Limatanthauza Chiyani?

Kodi “Alefa ndi Omega ndi Ndani”?

N’chifukwa chiyani dzina limeneli ndi loyenera?

Kodi Yerusalemu Watsopano N’chiyani?

Kodi mzinda umenewu uli ndi ubwino wotani kwa inu?

Kodi Chilombo cha Mitu 7 Chotchulidwa M’buku la Chivumbulutso Chaputala 13, Chikuimira Chiyani?

Chilombo chili ndi ulamuliro, mphamvu komanso mpando wachifumu. Kodi ulosi wa m’Baibulo umanenanso zotani zokhudza chilombochi?

Kodi Chilombo Chofiira Kwambiri Chomwe Chimatchulidwa M’chaputala 17 cha Chivumbulutso Chimaimira Chiyani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mfundo 6 zimene zingakuthandizeni kudziwa chilombo chotchulidwa mu chivumbulutso chaputala 17.

Kodi Nambala ya 666 Imatanthauza Chiyani?

Baibulo limatithandiza kudziwa tanthauzo la nambala ya 666 komanso chizindikiro cha chilombo.

Kodi Babulo Wamkulu N’chiyani?

Baibulo limanena kuti Babulo Wamkulu amatchedwanso kuti hule ndi mzinda.

Kodi Nyanja ya Moto N’chiyani? Kodi ndi Yofanana ndi Gehena?

Yesu ali ndi “makiyi a manda,” koma alibe makiyi a kunyanja ya moto?

Kodi Munthu Wachuma Komanso Lazaro Anali Ndani?

Kodi fanizo limene Yesu anafotokozali limatiphunzitsa kuti anthu abwino amapita kumwamba komanso kuti oipa amakazunzidwa ku moto wa ku gehena?

Kutha kwa Dziko

Kodi Chizindikiro cha “Masiku Otsiriza” Kapena Kuti Nthawi “ya Mapeto” N’chiyani?

Baibulo linaneneratu zinthu zambiri zomwe zidzachitika pa nthawi yofanana pokwaniritsa chizindikiro cha masiku otsiriza.

Kodi Baibulo Linaneneratu za Mmene Anthu Adzidzaganizira ndi Kuchitira Zinthu Masiku Ano?

Baibulo linaneneratu kuti anthu adzasintha n’kuyamba kukhala ndi makhalidwe oipa.

Kodi Chisautso Chachikulu N’chiyani?

Maulosi a m’Baibulo onena za nthawi yamapeto amati padziko padzakhala mavuto aakulu kwambiri omwe sanachitikepo. Kodi chidzachitike ndi chani pa nthawiyo?

Kodi Nkhondo ya Aramagedo Idzakhala Yotani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibulo, koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imatchulidwa m’Baibulo lonse.

Kodi Dzikoli Lidzatha?

Baibulo limafotokoza bwino chifukwa chimene Mulungu analengera dziko lapansili

Kodi Mapeto a Dzikoli Adzafika Liti?

Kuti tipeze yankho la funsoli, tiyenera kumvetsa zimene Baibulo limanena kuti zidzatha pa nthawiyo.

Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Chiyani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene zidzachitike boma la Mulungu likadzayamba kulamulira dziko lapansili.

Anthu, Malo ndi Zinthu

Kodi Tingaphunzire Chiyani kwa Akazi Otchulidwa m’Baibulo?

Onani kusiyana pakati pa akazi a zitsanzo zabwino otchulidwa m’Baibulo ndi ena omwe anali ndi makhalidwe oipa.

Kodi Mariya Ndi Amayi a Mulungu?

Malemba komanso mbiri yonena za mmene Chikhristu chinayambira zimatithandiza kudziwa zoona zokhudza chiphunzitso chimenechi.

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Zotani Zokhudza Mariya Virigo?

Ena amanena kuti Mariya sanabadwe ndi tchimo lililonse. Kodi Baibulo limati chiyani za nkhaniyi?

Kodi Yohane M’batizi Anali Ndani?

Uthenga wake umene unanenedweratu unakonzekeretsa mitima ya Ayuda anzake kuti azindikire Mesiya wolonjezedwa.

Kodi Mariya Mmagadala Anali Ndani?

Zinthu zina zimene anthu amakhulupirira zokhudza Mariya zilibe umboni m’Malemba.

Kodi “Anzeru a Kum’mawa” Anali Ndani? Kodi Mulungu Ndi Amene Anawachititsa Kuti Alondole Nyenyezi ya ku Betelehemu?

Miyambo yambiri yomwe imachitika yokhudza Khirisimasi siipezeka n’komwe m’Baibulo.

Kodi Baibulo Limanena Zotani Zokhudza Danieli?

Mulungu anamuonetsa masomphenya a zochitika zomwe zikukwaniritsidwa masiku athu ano.

Kodi Mkazi wa Kaini Anali Ndani?

Kuganizira mfundo za m’Malemba kumathandiza kupeza yankho logwira mtima la funso limeneli.

Kodi Nkhani ya Nowa Komanso Chigumula Ndi Nthano Chabe?

Baibulo limafotokoza kuti Mulungu anabweretsa chigumula kuti awononge anthu oipa. Kodi Baibulo lili ndi umboni wotani wotsimikizira kuti linalembedwadi ndi Mulungu?

Kodi Likasa la Pangano N’chiyani?

Mulungu analamula Aisiraeli akale kuti alipange. Kodi cholinga chake chinali chiyani?

Kodi Yesu Atafa Anakulungidwa mu Nsalu ya Maliro Yomwe Inasungidwa ku Turin?

Mfundo zitatu zofunika kwambiri zokhudza nsalu ya maliro zomwe zingatithandize kupeza mayankho.

Kodi Baibulo Limanena Zotani Zokhudza Nyama Zotchedwa Madainaso?

Kodi zomwe limanena zimagwirizana ndi sayansi?

Kodi Mulungu Anasintha Zamoyo Zina Polenga Mitundu Inanso ya Zamoyo?

Baibulo silitsutsa zimene asayansi amanena zoti mitundu ya zamoyo imatulutsanso zamoyo zina zofanana ndi zamtundu womwewo.

Malangizo Othandiza

Kodi Baibulo Lingandithandize kuti Ndikhale ndi Banja Losangalala?

Malangizo anzeru ochokera m’Baibulo athandiza kale anthu mamiliyoni ambirimbiri kukhala ndi mabanja osangalala.

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yokhala ndi Anzathu?

Anzathu abwino angatithandize kukhala anthu abwino. Tiyenera kusankha anzathu mwanzeru.

Kodi Yesu Anapereka Lamulo Lotani Lokhudza Kuchita Zinthu ndi Ena?

Pamene Yesu anapereka lamuloli, ankanena za mmene tiyenera kuchitira zinthu ndi anthu onse, ngakhale adani athu.

Kodi “Kukonda Adani Anu” Kumatanthauza Chiyani”?

Mawu a Yesu osavuta kumva koma amphamvu amene Yesu ananena angakhale ovuta kwambiri kuwachita.

Kodi Ndingatani Kuti Ndizisankha Zochita Mwanzeru?

Mfundo 6 za m’Baibulo zingakuthandizeni kupeza nzeru komanso kumvetsa zinthu.

Kodi Chiyembekezo Ndingachipeze Kuti?

Malangizo odalirika angakuthandizeni kuti muzisangalala komanso kuti muziyembekezera zinthu zabwino mtsogolo.

Kodi Ndalama ndi Zimene Zimabweretsa Mavuto Onse?

Zimene anthu ambiri amakonda kunena zoti “ndalama ndi muzu wa zoipa zonse,” zimangosonyeza kuti samvetsa zimene Baibulo limafotokoza.

Kodi Baibulo Lingathandize pa Nkhani ya Mavuto Azachuma Ndiponso Ngongole?

Ndalama sizingakuthandizeni kukhala wosangalala koma pali mfundo za m’Baibulo zinayi zimene zingakuthandizeni pa mavuto azachuma.

Kodi Baibulo Lingandithandize Kupirira Matenda?

Inde. Onani mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kuti mupirire matenda.

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Kubwezera?

Malangizo a m’Baibulo athandiza anthu ambiri kuti athetse mtima wofuna kubwezera.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kukwiya?

Kodi pali zifukwa zomveka zoti munthu angakwiyire? Nanga angatani ngati mkwiyowo wayamba kukula?

Kodi Baibulo Lingandithandize Ngati Ndili ndi Nkhawa?

Pali zinthu zitatu zimene Mulungu amapereka kuti athandize anthu amene ali ndi nkhawa.

Kodi Chipembedzo, Mulungu Kapena Baibulo Zingandithandize Kuti Ndikhale Wosangalala?

Onani mmene kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu kungakuthandizireni kukhala wosangalala panopa komanso m’tsogolo muno.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yodzikonda Wekha?

Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ankanena kuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha?”