Pitani ku nkhani yake

Ufumu wa Mulungu

Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?

Dziwani chifukwa chake Ufumu wa Mulungu uli woposa boma lililonse la anthu.

Kodi Ufumu wa Mulungu Uli Mumtima Mwanu?

Kodi mawu a m’Baibulo akuti “ufumu wa Mulungu uli pakati panu” akutanthauza chiyani?

Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Chiyani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene zidzachitike boma la Mulungu likadzayamba kulamulira dziko lapansili.

Kodi Ulosi wa M’Baibulo Umatiuza Zotani pa Nkhani ya Chaka cha 1914?

Ulosi wa “nthawi zokwanira 7” wopezeka mu Danieli chaputala 4 umasonyeza nthawi yapadera yokhudza ulamuliro wa anthu.

Kodi “Makiyi a Ufumu” N’chiyani?

Kodi makiyiwa anatsegula chiyani, nanga anagwiritsidwa ntchito pothandiza ndani? Kodi ndi ndani amene anatsegula?