Pitani ku nkhani yake

Makhalidwe

Ukwati Komanso Mabanja

Kodi Baibulo Lingandithandize kuti Ndikhale ndi Banja Losangalala?

Malangizo anzeru ochokera m’Baibulo athandiza kale anthu mamiliyoni ambirimbiri kukhala ndi mabanja osangalala.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Banja?

Mfundo za m’Baibulo zingathandize mwamuna ndi mkazi wake kuti apewe kapenanso kuthetsa mavuto am’banja lawo.

Kodi Baibulo Limavomereza Kuti Mwamuna ndi Mkazi Azikhalira Limodzi Asanakwatirane?

Malangizo ochokera kwa Mulungu amatithandiza kudziwa zimene tingachite kuti tikhale ndi banja logwirizana ndipo anthu amene amatsatira mfundo zake zinthu zimawayendera bwino nthawi zonse.

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Ukwati wa Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Mulungu amene anayambitsa ukwati amadziwa bwino zimene anthu okwatirana angachite kuti akhale ndi banja lolimba komanso losangalala.

Kodi Baibulo Limaloleza Kuthetsa Ukwati?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Mulungu amaloleza komanso zimene amadana nazo.

Kodi Mulungu Amaloleza Mitala?

Kodi Mulungu ndi amene anayambitsa mitala? Taonani zimene Baibulo limanena pa nkhani imeneyi.

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yokwatirana ndi Munthu wa Mtundu Wina?

Onani mfundo zina za m’Baibulo zimene zingathandize pa nkhani ya kusiyana mitundu ndiponso ukwati.

Kodi Munthu Angasonyeze Bwanji Kuti ‘Amalemekeza Bambo Ake ndi Mayi Ake’?

Mukhoza kudabwa kudziwa zimene lamuloli silitanthauza.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yosamalira Makolo Achikulire?

Baibulo limafotokoza zimene amuna ndi akazi ena anachita m’mbuyomo posamalira makolo awo achikulire. Lilinso ndi mfundo zomwe zingathandize anthu omwe akusamalira makolo achikulire panopa.

Kugonana

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Kodi Mulungu amaona bwanji anthu ogonana amuna kapena akazi okhaokha? Kodi zingatheke kuti munthu amene ali ndi mtima wofuna kugonana ndi amuna kapena akazi anzake ayambe kuchita zinthu zosangalatsa Mulungu?

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Zolaula Ndiponso Kukambirana Zokhudza Kugonana pa Intaneti?

Masiku ano, mavidiyo, mabuku, nyimbo ngakhalenso zithunzi zolaula zachuluka kwambiri. Kodi zimenezi zilibe vuto lililonse?

Kodi Baibulo Limaletsa Kugonana?

Kodi kugonana ndi tchimo?

Kodi Akhristu Ayenera kugwiritsa Ntchito Njira Zakulera?

Pa nkhani yogwiritsa ntchito njira zakulera, kodi pali lamulo la m’Baibulo limene mwamuna ndi mkazi wake ayenera kuliganizira?

Kodi Ndingatani Kuti Anthu Ena Asamandichitire Zachipongwe?

Mfundo 7 zogwirizana ndi zimene Baibulo limanena, zingakuthandizeni kupirira anthu ena akamakuchitirani zachipongwe kapena kukukamizani kuti mugone nawo.

Kodi Makolo Angatani Kuti Aphunzitse Ana Awo Nkhani Zokhudza Kugonana?

M’Baibulo muli mfundo zambiri zimene zingakuthandizeni mukafuna kuphunzitsa ana anu mmene angadzitetezere kwa anthu ogwiririra.

Zimene Timasankha

Kodi Mkhristu Angalandire Chithandizo cha Mankhwala Akadwala?

Kodi chithandizo chimene tingasankhe chimakhudza ubwenzi wathu ndi Mulungu?

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yoikidwa Magazi?

M’Baibulo, Mulungu anapereka lamulo lakuti ‘tizipewa magazi.’ Kodi tingatani kuti titsatire lamulo limeneli masiku ano?

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yochotsa Mimba?

Kodi moyo wa munthu umayamba liti? Kodi Mulungu angakhululukire munthu amene anachotsapo mimba?

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yodzilemba Matatuu?

Kodi matatuu amakusangalatsani? Kodi ndi mfundo ziti za m’Baibulo zimene muyenera kuziganizira?

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Kudziphoda Komanso Kuvala Zodzikongoletsera?

Kodi Malemba amaletsa kudziphoda ndi kuvala zodzikongoletsera?

Kodi Baibulo Limanena Kuti Kumwa Mowa Ndi Tchimo?

Baibulo limasonyeza kuti mowa ukhoza kuthandiza munthu amene akudwala m’mimba komanso likhoza kuthandiza munthu kuti azisangalala.

Kodi Kusuta Ndi Tchimo?

Popeza kuti m’Baibulo mulibemo nkhani yokhudza kusuta, ndiye zingatheke bwanji kuti liyankhe funso limeneli?

Kodi Baibulo Limati Mungasankhe Nokha Zochita Kapena Mulungu Analemberatu Tsogolo Lanu?

Anthu ambiri amakhulupirira kuti Mulungu analemberatu tsogolo lathu. Kodi zimene timasankha zimakhudza tsogolo lathu?

Kodi Ndingatani Kuti Ndizisankha Zochita Mwanzeru?

Mfundo 6 za m’Baibulo zingakuthandizeni kupeza nzeru komanso kumvetsa zinthu.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kupatsa?

Kodi Mulungu amasangalala ndi kupatsa kotani?