Pitani ku nkhani yake

Kuvutika

N'chifukwa Chiyani Anthu Akuvutika Chonchi?

Kodi Mulungu Ndi Amene Amachititsa Kuti Tizivutika?

N’chifukwa chiyani munthu aliyense amavutika, ngakhale amene Mulungu amamukonda?

Kodi Mdyerekezi Ndi Amene Amachititsa Mavuto Onse?

Baibulo limanena chifukwa chimene chimachititsa kuti anthufe tizivutika.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Ngozi Zadzidzidzi?

Kodi ngozi zadzidzidzi ndi chilango chochokera kwa Mulungu? Kodi Mulungu amathandiza bwanji anthu amene akhudzidwa ndi ngozi zadzidzidzi?

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Miliri?

Anthu ena amanena kuti Mulungu akugwiritsa ntchito miliri ndi matenda ena polanga anthu masiku ano. Koma zimenezi n’zosagwirizana ndi zimene Baibulo limanena.

N’chifukwa Chiyani Mulungu Analola Kuti Anthu Ambirimbiri Aphedwe mu Ulamuliro wa Nazi ku Germany?

Anthu ambiri amafunsa chifukwa chake Mulungu yemwe ndi wachikondi amalola kuti anthu azivutika. Baibulo limapereka mayankho omveka bwino

N’chifukwa Chiyani Mtendere Ndi Wosowa M’dzikoli?

Anthu alephera kubweretsa mtendere. Taonani zifukwa zingapo zimene zikuchititsa kuti anthu azilephera kubweretsa mtendere.

Kupirira Mavuto

Kodi M’Baibulo Mungapezemo Mawu Omwe Angakulimbikitseni?

Mawu a m’Baibulo alimbikitsa anthu ambiri omwe akulimbana ndi mavuto ena ake komanso omwe amavutika maganizo chifukwa cha mavuto.

Kodi Baibulo Lingandithandize Ngati Ndili ndi Nkhawa?

Pali zinthu zitatu zimene Mulungu amapereka kuti athandize anthu amene ali ndi nkhawa.

Kodi Baibulo Lingandithandize Ngati Ndili ndi Maganizo Ofuna Kudzipha?

Kodi Baibulo limapereka malangizo otani kwa munthu amene akufuna kudzipha?

Kodi Baibulo Lingandithandize Kupirira Matenda?

Inde. Onani mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kuti mupirire matenda.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yomalizitsa Munthu Amene Akuvutika Kwambiri ndi Ululu?

Bwanji ngati zadziwika kuti munthuyo sachira, kodi pali vuto ndi kutalikitsako moyo wake?

Mavuto Onse Adzatha

Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Chiyani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene zidzachitike boma la Mulungu likadzayamba kulamulira dziko lapansili.

Kodi Chiyembekezo Ndingachipeze Kuti?

Malangizo odalirika angakuthandizeni kuti muzisangalala komanso kuti muziyembekezera zinthu zabwino mtsogolo.