Pitani ku nkhani yake

Kumwamba

Kumwamba

Kodi Mawu Akuti Kumwamba Amatanthauza Chiyani?

Malinga ndi zimene Baibulo limanena, mawuwa amagwiritsidwa ntchito poimira zinthu zitatu.

Kodi Ndi Ndani Amene Amapita Kumwamba?

Anthu ambiri amaganiza kuti anthu onse abwino amapita kumwamba. Koma kodi Baibulo limaphunzitsa chiyani pa nkhaniyi?

Kodi Yerusalemu Watsopano N’chiyani?

Kodi mzinda umenewu uli ndi ubwino wotani kwa inu?

Kodi Mulungu Ali ndi Malo Enieni Amene Amakhala?

Kodi Baibulo limati Mulungu amakhala kuti? Kodi Yesu amakhala kumene kuli Mulungu?

Angelo

Kodi Angelo Ndi Otani?

Kodi angelo alipo angati? Kodi ali ndi mayina komanso ndi osiyanasiyana?

Kodi Mikayeli Mkulu wa Angelo Ndi Ndani?

Amadziwika ndi dzina lina limene mumalidziwa bwino.

Satana ndi Ziwanda

Kodi Mdyerekezi Alipodi?

Kodi Mdyerekezi ndi uchimo umene umakhala mumtima mwa munthu kapena ndi mngelo woti alipodi?

Kodi Mulungu Analenga Mdyerekezi Kuti Azitiyesa?

Kodi Satana anachokera kuti? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake Yesu ananena kuti Mdyerekezi “sanakhazikike m’choonadi.”

Kodi Mdyerekezi Amakhala Kuti?

Baibulo limanena kuti Mdyerekezi anachotsedwa kumwamba. Ndiye panopa akukhala kuti?

Kodi Mdyerekezi Angalamulire Zochita za Anthu?

Kodi Mdyerekezi amakola bwanji anthu, ndipo ifeyo tingatani kuti tisakodwe ndi misampha yake?

Kodi Mdyerekezi Ndi Amene Amachititsa Mavuto Onse?

Baibulo limanena chifukwa chimene chimachititsa kuti anthufe tizivutika.

Kodi Ziwanda Zilipodi?

Kodi ziwanda ndi chani? Kodi zinachokera kuti?

Kodi Anefili Anali Ndani?

Baibulo limafotokoza kuti anali “ziphona zakalelo, amuna otchuka.” Kodi timadziwa zotani zokhudza Anefili?