Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2013 Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2013 CHIPEMBEDZO Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu? 8/13 KUCHEZA NDI ANTHU Dokotala Woona za Mafupa (Hof Laurenceau, I.), 8/13 Katswiri wa Impso (Granolleras, C.), 9/13 Katswiri Woimba Piyano (Nebolsin, E.), 11/13 Katswiri Wopanga Maloboti (Tistarelli, M.), 2/13 Mzimayi Wachiyuda (Hall R. ), 5/13 “Sakayikira Zoti Mulungu Analenga Zamoyo Zonse” (Schenck, B.), 4/13 Wasayansi ya mmene zinthu zinapangidwira (Loos, D.), 10/13 Wasayansi yofufuza mmene maselo a m’thupi amagwirira ntchito (Chiozzi, P.), 1/13 MAUNANSI A ANTHU Bambo Wabwino, 3/13 Khazikitsani Malamulo Oti Mwana Wanu Azitsatira, 3/13 Kudzivulaza Mwadala, 8/13 Kulera Ana Kuti Asakhale Odzikonda, 1/13 Kuthetsa Nkhanza za M’banja, 4/13 Kutumizirana Zinthu Zolaula, 11/13 Makhalidwe Othandiza Kuti Muzisangalala, 11/13 Mawu Achipongwe, 4/13 Mungatani Kuti Muzikhululukirana? 9/13 Mungatani Kuti Muzimasukirana ndi Mwana Wanu, 1/13 Muzimvetsera, 12/13 Mwana Akayamba Kuvuta, 7/13 Ngati Mumacheza Kwambiri ndi Munthu Amene si Mwamuna Kapena Mkazi Wanu, 10/13 Zimene Mungachite Kuti Musamakangane, 2/13 Zimene Mungachite Kuti Musamasiye Kulankhulana Mukasemphana Maganizo, 6/13 Zimene Mungachite Kuti Mwana Wanu Azikumverani, 5/13 MAYIKO NDI ANTHU Azerbaijan, 7/13 Brazil, 12/13 Cameroon, 1/13 Indonesia, 4/13 Panama, 6/13 MBONI ZA YEHOVA Mukhoza Kulowa pa Webusaiti Yathu Mosavuta 4/13 NYAMA NDI ZOMERA Agulugufe, 12/13 Mphaka wa M’tchire, 7/13 Mphalapala, 3/13 SAYANSI Chigoba Chomwenso Chimaona, 5/13 Gologolo wa Ubongo Wodabwitsa Kwambiri, 7/13 Khutu Lamphamvu la Bwamnoni, 10/13 Kuchuluka kwa Zinthu Zimene DNA Imasunga, 12/13 Maso a Kangaude, 3/13 Mbalame ya Albatross Yosatopa ndi Kuuluka, 8/13 Mbalame Yotha Kuuluka Ulendo Wautali, 1/13 Mchira wa Gulo, 2/13 Nthenga za Mbalame Zochititsa Chidwi Kwambiri, 9/13 Zipsepse za Nangumi, 6/13 UMOYO NDI MANKHWALA Khunyu, 10/13 Kodi N’zotheka Kukhala Ndi Moyo Wautali? 8/13 Kusiya Kusamba, 11/13 ZACHUMA NDI NTCHITO Kugula Zinthu Mwachisawawa 6/13 ZIMENE BAIBULO LIMANENA Anthu Ovutika, 2/13 Banja, 11/13 Kugonana Musanakwatirane, 9/13 Kuvutika Maganizo, 10/13 Mmene Mulungu Alili, 5/13 Mowa, 8/13 Paradaiso, 1/13 Satana, 6/13 Thanzi Lathu, 4/13 Ufumu wa Mulungu, 7/13 Yesu, 12/13 Zolaula, 3/13 ANTHU AKALE Boyle, Robert, 3/13 Koresi Wamkulu, 5/13 Plato, 2/13 Zheng He, 9/13 ZOCHITIKA PADZIKO Chenjerani ndi Mbava Komanso Anthu Ogwiririra, 5/13 Kodi Ofalitsa Nkhani Tingawakhulupirire? 12/13 Kodi Osamukira Kudziko Lina Amakapezadi Zimene Akufuna? 2/13 Kodi Zionetsero Zimathetsadi Mavuto? 7/13 ZOSIYANASIYANA Halowini, 9/13 Kodi Mumachita “Phwando Nthawi Zonse”? 11/13 Kupha Anthu M’dzina la Mulungu 6/13 Zinthu Zimene Sitingagule ndi Ndalama, 10/13 Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2013 GALAMUKANI! Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2013 Chichewa Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2013