Koperani chithunzi cha Yosefe. Lembani zinthu zitatu zimene zikusowapo, lumikizani timadonthoto kenako chikongoletseni ndi chekeni.