Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mukhoza Kulowa pa Webusaiti Yathu Mosavuta

Mukhoza Kulowa pa Webusaiti Yathu Mosavuta

Kuyambira ndi Galamukani! ino ya mwezi wa April, magazini ya Galamukani! izikhala ndi kachidindo kotchedwa QR (quick response). Kachidindo kameneka kazikhala ndi manambala osaoneka omwe azithandiza munthu kulowa pa Webusaiti yathu mosavuta. Mungathe kugwiritsa ntchito njira imeneyi ngati muli ndi foni yapamwamba yokhala ndi kamera komanso Intaneti.

  1. Pangani dawunilodi pulogalamu yomwe imatha kuzindikira manambala a QR.

  2. Tsegulani pulogalamuyo.

  3. Jambulani kachidindo ka QR.

Nthawi yomweyo foni yanu itsegula Webusaiti yathu.