Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Mika

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7

Mitu

  • 1

    • Chiweruzo cha Samariya ndi Yuda (1-16)

      • Machimo ndi kugalukira zinabweretsa mavuto (5)

  • 2

    • Tsoka kwa opondereza anzawo (1-11)

    • Aisiraeli anagwirizanitsidwa (12, 13)

      • Mʼdziko mudzadzaza phokoso la anthu (12)

  • 3

    • Atsogoleri ndi aneneri anadzudzulidwa (1-12)

      • Mika anapatsidwa mphamvu ndi mzimu wa Yehova (8)

      • Ansembe ankaphunzitsa kuti apeze ndalama (11)

      • Yerusalemu adzakhala bwinja (12)

  • 4

    • Phiri la Yehova lidzakwezedwa (1-5)

      • Kusula malupanga kuti akhale makasu a pulawo (3)

      • ‘Ife tidzayenda mʼdzina la Yehova’ (5)

    • Ziyoni adzakhalanso wamphamvu (6-13)

  • 5

    • Wolamulira amene adzakhale wamphamvu padziko lonse (1-6)

      • Wolamulira adzachokera ku Betelehemu (2)

    • Anthu otsala adzakhala ngati mame komanso mkango (7-9)

    • Dziko lidzayeretsedwa (10-15)

  • 6

    • Mulungu anaimba mlandu Aisiraeli (1-5)

    • Yehova akufuna kuti uzichita chiyani? (6-8)

      • Chilungamo, kukhulupirika, kudzichepetsa (8)

    • Aisiraeli analakwa nʼkulangidwa (9-16)

  • 7

    • Makhalidwe oipa a Aisiraeli (1-6)

      • Adani a munthu adzakhala anthu a mʼbanja lake (6)

    • “Ine ndidzayembekezera Yehova” (7)

    • Anthu a Mulungu zinthu zidzawayendera bwino (8-13)

    • Mika anapemphera komanso kutamanda Mulungu (14-20)

      • Yehova anayankha (15-17)

      • ‘Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi Yehova?’ (18)