Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B12-A

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 1)

Yerusalemu ndi Madera Ozungulira

 1. Kachisi

 2. Munda wa Getsemane (?)

 3. Nyumba ya Bwanamkubwa

 4. Nyumba ya Kayafa (?)

 5. Nyumba imene Herode Antipa ankakhala (?)

 6. Damu la Betizata

 7. Dziwe la Siloamu

 8. Holo ya Khoti Lalikulu la Ayuda (?)

 9. Gologota (?)

 10. Munda Wamagazi (?)

    Sankhani tsiku:  Nisani 8 |  Nisani 9 |  Nisani 10 |  Nisani 11

 Nisani 8 (Sabata)

MADZULO (Masiku a Ayuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)

 • Anafika ku Betaniya kutatsala masiku 6 kuti Pasika achitike

M’MAWA

MADZULO

 Nisani 9

MADZULO

 • Anakadya kunyumba ya Simoni wakhate

 • Mariya anadzoza Yesu mafuta a nado

 • Ayuda anabwera kudzaona Yesu ndi Lazaro

M’MAWA

 • Analowa mu Yerusalemu ndipo anthu anasangalala

 • Anaphunzitsa m’kachisi

MADZULO

 Nisani 10

MADZULO

 • Anakhala usiku wonse ku Betaniya

M’MAWA

 • Analawirira kupita ku Yerusalemu

 • Anathamangitsa ogulitsa malonda m’kachisi

 • Yehova analankhula kuchokera kumwamba

MADZULO

 Nisani 11

MADZULO

M’MAWA

 • Anaphunzitsa m’kachisi pogwiritsa ntchito mafanizo

 • Anadzudzula Afarisi mwamphamvu

 • Anaona mkazi wamasiye akuponya timakobidi tiwiri

 • Paphiri la Maolivi, ananeneratu za kuwonongedwa kwa Yerusalemu ndi chizindikiro cha kukhalapo kwake

MADZULO