Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B11

Kachisi Wapaphiri mu Nthawi ya Yesu

 1. Mbali za Kachisi

 2. 1 Malo Oyera Koposa

 3. 2 Malo Oyera

 4. 3 Guwa Lansembe Zopsereza

 5. 4 Thanki Yosungira Madzi

 6. 5 Bwalo la Ansembe

 7. 6 Bwalo la Aisiraeli

 8. 7 Bwalo la Akazi

 9. 8 Bwalo la Anthu a Mitundu Ina

 10. 9 Chotchinga (Khoma lamiyala)

 11. 10 Khonde la Mafumu

 12. 11 Khonde Lazipilala la Solomo

 13. 12 Nyumba Yachitetezo ya Antonia