A7-B
Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Chiyambi cha Utumiki wa Yesu
NTHAWI |
MALO |
ZIMENE ZINACHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
29, chakumapeto kwa chaka |
Mtsinje wa Yorodano kapena ku Betaniya wakutsidya la Yorodano |
Ubatizo ndi kudzozedwa kwa Yesu; Yehova analengeza kuti Yesu ndi Mwana wake ndipo anamuvomereza |
||||
Chipululu cha Yudeya |
Yesu ayesedwa ndi Mdyerekezi |
|||||
Betaniya wakutsidya lina la Yorodano |
Yohane Mʼbatizi ananena kuti Yesu ndi Mwanawankhosa wa Mulungu; ophunzira oyambirira anatsatira Yesu |
|||||
Kana wa ku Galileya; Kaperenao |
Chozizwitsa choyamba, madzi anawasandutsa vinyo; anapita ku Kaperenao |
|||||
30, Pasika |
Yerusalemu |
Anayeretsa kachisi |
||||
Yesu anakambirana ndi Nikodemo |
||||||
Yudeya; Ainoni |
Anapita kumidzi ya ku Yudeya, ophunzira ake anabatiza anthu; Ulaliki womaliza wa Yohane wokhudza Yesu |
|||||
Tiberiyo; Yudeya |
Yohane anaikidwa mʼndende; Yesu ananyamuka kupita ku Galileya |
|||||
Sukari, ku Samariya |
Ali pa ulendo wopita ku Galileya, anaphunzitsa Asamariya |
Chipululu cha Yudeya