Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

FUNSO 4

Kodi Baibulo Ndi Lolondola pa Nkhani Zasayansi?

“Iye anatambasula thambo lakumpoto pamwamba pa malo opanda kanthu, ndipo dziko lapansi analiika mʼmalere.”

Yobu 26:7

“Mitsinje yonse imakathira mʼnyanja koma nyanjayo sidzaza. Imabwerera kumalo kumene ikuchokera kuti ikayambirenso kuyenda.”

Mlaliki 1:7

“Pali winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi.”

Yesaya 40:22