B14-B
Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu
Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu MʼMalemba a Chiheberi
|
Gera (1⁄20 ya sekeli) Magalamu 0.57 Magera 10 = Beka imodzi |
|
Beka Magalamu 5.7 Mabeka awiri = Sekeli imodzi |
|
Pimu Magalamu 7.8 Pimu imodzi = 2⁄3 ya sekeli |
|
Kulemera kwa sekeli Sekeli Magalamu 11.4 Masekeli 50 = Mina imodzi |
|
Mina Magalamu 570 Ma mina 60 = Talente imodzi |
|
Talente Makilogalamu 34.2 |
|
Dariki (ya ku Perisiya, yagolide) Magalamu 8.4 |
Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu MʼMalemba a Chigiriki
|
Leputoni (ya Ayuda, yamkuwa) 1⁄2 ya kwadiransi |
|
Kwadiransi (ya Aroma, yamkuwa) Maleputa awiri |
|
Asariyoni (ya Aroma ndi madera ozungulira, yamkuwa) Makwadiransi 4 |
|
Dinari (ya Aroma, yasiliva) Makwadiransi 64 Magalamu 3.85 Malipiro a Tsiku Limodzi (Maola 12) Malipiro a Masiku Awiri |
|
Dalakima (ya Agiriki, yasiliva) Magalamu 3.4 Malipiro a Tsiku Limodzi (Maola 12) |
|
Didalakima (ya Agiriki, yasiliva) Madalakima awiri Magalamu 6.8 Malipiro a Masiku Atatu |
|
Tetiradalakima ya ku Antiokeya Tetiradalakima ya ku Turo (Sekeli yasiliva ya ku Turo) Tetiradalakima (ya Agiriki, yasiliva; imatchedwanso siteta yasiliva) Madalakima 4 Magalamu 13.6 Malipiro a Masiku 4 |
|
Mina Madalakima 100 Magalamu 340 = Malipiro a masiku pafupifupi 100 |
|
Talente Ma mina 60 Makilogalamu 20.4 = Malipiro a zaka pafupifupi 20 |
|
Paundi (ya Aroma) Magalamu 327
|

