Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B15

Kalendala ya Chiheberi

NISANI (ABIBU) March—April

14 Pasika

15-21 Mkate Wopanda Zofufumitsa

16 Nsembe ya zipatso zoyamba kucha

Yorodano ankasefukira chifukwa cha mvula ndi madzi osungunuka

Balere

IYARA (ZIVI) April—May

14 Pasika Wochitika Nthawi Yake Itadutsa

Nthawi ya chilimwe, kumwamba kopanda mitambo

Tirigu

SIVANI May—June

6 Chikondwerero cha Masabata (Pentekosite)

Kunja kunkatentha koma kunkakhala mpweya wabwino

Tirigu, nkhuyu zoyambirira

TAMUZI June—July

 

Kutentha kunkawonjezereka, mame ankagwa ambiri

Mphesa zoyambirira

ABI July—August

 

Kutentha kunkafika pachimake

Zipatso zamʼchilimwe

ELULI August—September

 

Kutentha kunkapitirira

Kanjedza, mphesa ndi nkhuyu

TISHIRI (ETANIMU) September—October

1 Tsiku loliza lipenga

10 Mwambo Wophimba Machimo

15-21 Chikondwerero cha Misasa

22 Msonkhano wapadera

Chilimwe chikutha, mvula ikuyamba

Kulima

HESHIVANI (BULI) October—November

 

Mvula yowaza—

Maolivi

KISILEVI November—December

25 Chikondwerero cha Kupereka Kachisi wa Mulungu

Mvula inkawonjezereka, madzi ankaundana mʼmapiri

Nyengo yozizira ziweto zinkakhala mʼkhola

TEBETI December—January

 

Kunkazizira kwambiri, kunkagwa mvula, madzi ankaundana mʼmapiri

Zomera zikukula

SEBATI January—February

 

Kuzizira kunkacheperako, mvula inkapitiriza kugwa

Amondi ankachita maluwa

ADARA February—March

14, 15 Purimu

Kunkachitika mabingu, kunkagwa mvula yamatalala

Fulakesi

VEADARA March

Pa zaka 19 zilizonse, zaka 7 zinkakhala ndi mwezi wowonjezera