Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B9

Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Amene Danieli Analosera

Babulo

Danieli 2:32, 36-38; 7:4

Mfumu Nebukadinezara anawononga Yerusalemu mu 607 B.C.E.

Mediya ndi Perisiya

Danieli 2:32, 39; 7:5

Anagonjetsa Babulo mu 539 B.C.E.

Koresi analamula kuti Ayuda abwerere ku Yerusalemu mu 537 B.C.E.

Girisi

Danieli 2:32, 39; 7:6

Alekizanda Wamkulu anagonjetsa Perisiya mu 331 B.C.E.

Roma

Danieli 2:33, 40; 7:7

Anayamba kulamulira Isiraeli mu 63 B.C.E.

Anawononga Yerusalemu mu 70 C.E.

Britain ndi America

Danieli 2:33, 41-43

Mu 1914-1918 C.E. Mayiko a Britain ndi America anayamba kulamulira dziko lonse mkati mwa Nkhondo Yoyamba ya Padziko Lonse