BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023)

Kodi Mungatani Kuti Muzipindula Kwambiri Mukamawerenga Baibulo?

Chichewa
Kodi Mungatani Kuti Muzipindula Kwambiri Mukamawerenga Baibulo?
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt p. 36

FUNSO 20

Kodi Mungatani Kuti Muzipindula Kwambiri Mukamawerenga Baibulo?

MUKAMAWERENGA BAIBULO MUZIDZIFUNSA MAFUNSO AWA:

Kodi ndikuphunzirapo chiyani zokhudza Yehova Mulungu?

Kodi malembawa akugwirizana bwanji ndi uthenga wa mʼBaibulo lonse?

Kodi zimene ndawerengazi ndingazigwiritse ntchito bwanji?

Kodi ndingagwiritse ntchito bwanji malembawa pothandiza anthu ena?

“Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga, komanso kuwala kounikira njira yanga.”

Salimo 119:105