DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Nyimbo ya Solomo Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 Kalata Yoyamba Yopita kwa Akorinto Machaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 Mitu 1 Mawu oyamba (1-3) Paulo anayamikira Mulungu chifukwa cha Akorinto (4-9) Anawalangiza kuti akhale ogwirizana (10-17) Khristu ndi mphamvu komanso nzeru ya Mulungu (18-25) Kudzitama mwa Yehova (26-31) 2 Paulo analalikira ku Korinto (1-5) Nzeru za Mulungu ndi zapamwamba (6-10) Kusiyana pakati pa munthu wauzimu ndi munthu wokonda za mʼdziko (11-16) 3 Akorinto ankakondabe zinthu za mʼdziko (1-4) Mulungu ndi amene amakulitsa (5-9) Antchito anzake a Mulungu (9) Kumanga ndi zinthu zosagwira moto (10-15) Ndinu kachisi wa Mulungu (16, 17) Nzeru zamʼdziko ndi zopusa kwa Mulungu (18-23) 4 Atumiki ayenera kukhala okhulupirika (1-5) Atumiki a Chikhristu ayenera kukhala odzichepetsa (6-13) ‘Musapitirire zolembedwa’ (6) Akhristu akuonetsedwa mʼbwalo lamasewera (9) Paulo ankasamalira ana ake auzimu (14-21) 5 Nkhani ya munthu yemwe anachita chiwerewere (1-5) Zofufumitsa zochepa zimafufumitsa mtanda wonse (6-8) Munthu woipa anayenera kuchotsedwa (9-13) 6 Akhristu ankatengerana kukhoti (1-8) Anthu amene sadzalowa mu Ufumu (9-11) Lemekezani Mulungu ndi matupi anu (12-20) “Thawani chiwerewere” (18) 7 Malangizo a anthu amene sali pabanja ndi amene ali pabanja (1-16) Mukhale mmene munalili pamene munkaitanidwa (17-24) Anthu omwe sali pabanja ndiponso akazi amasiye (25-40) Ubwino wosakhala pabanja (32-35) Kukwatiwa “mwa Ambuye” (39) 8 Chakudya choperekedwa kwa mafano (1-13) Kwa ife kuli Mulungu mmodzi (5, 6) 9 Chitsanzo cha mtumwi Paulo (1-27) “Usamange ngʼombe pakamwa” (9) ‘Tsoka kwa ine ngati sindilalikira’ (16) Kukhala zinthu zonse kwa anthu onse (19-23) Kudziletsa pa mpikisano wokalandira moyo (24-27) 10 Zitsanzo zotichenjeza za Aisiraeli (1-13) Chenjezo pa nkhani yolambira mafano (14-22) Tebulo la Yehova ndiponso tebulo la ziwanda (21) Ufulu ndiponso kuganizira ena (23-33) “Muzichita zinthu zonse kuti zibweretse ulemerero kwa Mulungu” (31) 11 “Muzitsanzira ine” (1) Nkhani yokhudza mutu ndiponso kuvala chophimba kumutu (2-16) Mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (17-34) 12 Mphatso za mzimu (1-11) Thupi limodzi, ziwalo zambiri (12-31) 13 Chikondi—njira yopambana (1-13) 14 Mphatso yonenera ndiponso yolankhula malilime (1-25) Misonkhano izichitika mwadongosolo (26-40) Zimene akazi ayenera kuchita mumpingo (34, 35) 15 Kuukitsidwa kwa Khristu (1-11) Kuuka kwa akufa ndi maziko a chikhulupiriro (12-19) Kuuka kwa Khristu kumatitsimikizira kuti akufa adzauka (20-34) Thupi la mnofu ndiponso thupi lauzimu (35-49) Thupi loti silingafe kapena kuwonongeka (50-57) Kuchita zambiri pa ntchito ya Ambuye (58) 16 Kutolera zopereka zopita kwa Akhristu a ku Yerusalemu (1-4) Maulendo amene Paulo ankafuna kuyenda (5-9) Ulendo wa Timoteyo ndiponso wa Apolo (10-12) Malangizo ndiponso kupereka moni (13-24) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena 1 Akorinto—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) 1 Akorinto—Zimene Zili Mʼbukuli Chichewa 1 Akorinto—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt 1 Corinthians pp. 1928-1929