BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023)

Rute—Zimene Zili Mʼbukuli

Chichewa
Rute—Zimene Zili Mʼbukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt Ruth

Buku la Rute

Machaputala

1 2 3 4

Mitu

  • 1

    • Banja la Elimeleki linasamukira ku Mowabu (1, 2)

    • Naomi, Olipa ndi Rute anakhala amasiye (3-6)

    • Rute anakhala wokhulupirika kwa Naomi ndi Mulungu wake (7-17)

    • Naomi anabwerera ku Betelehemu ndi Rute (18-22)

  • 2

    • Rute anakakunkha mʼmunda wa Boazi (1-3)

    • Rute anakumana ndi Boazi (4-16)

    • Rute anauza Naomi kuti Boazi anamukomera mtima (17-23)

  • 3

    • Naomi anapereka malangizo kwa Rute (1-4)

    • Rute ndi Boazi kopunthira mbewu (5-15)

    • Rute anabwerera kwa Naomi (16-18)

  • 4

    • Boazi anakhala wowombola (1-12)

    • Boazi ndi Rute anabereka Obedi (13-17)

    • Mzere wa makolo a Davide (18-22)