BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023)

Yuda—Zimene Zili Mʼbukuli

Chichewa
Yuda—Zimene Zili Mʼbukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt Jude

Kalata ya Yuda

Machaputala

1

Mitu

  • Moni (1, 2)

  • Aphunzitsi abodza adzaweruzidwa (3-16)

    • Mikayeli anakangana ndi Mdyerekezi (9)

    • Ulosi wa Inoki (14, 15)

  • Mupitirize kuchita zinthu zimene zingachititse kuti Mulungu azikukondani (17-23)

  • Mulungu ndi woyenera ulemerero (24, 25)