BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023)

Tito—Zimene Zili Mʼbukuli

Chichewa
Tito—Zimene Zili Mʼbukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt Titus

Kalata Yopita kwa Tito

Machaputala

1 2 3

Mitu

  • 1

    • Moni (1-4)

    • Tito aike akulu ku Kerete (5-9)

    • Kudzudzula anthu osalamulirika (10-16)

  • 2

    • Malangizo abwino kwa achinyamata ndi achikulire (1-15)

      • Kukana moyo wosaopa Mulungu (12)

      • Kudzipereka pa ntchito zabwino (14)

  • 3

    • Kugonjera koyenera (1-3)

    • Kukonzekera ntchito zabwino (4-8)

    • Kupewa mpatuko komanso kutsutsana pa zinthu zopusa (9-11)

    • Malangizo ena komanso moni (12-15)