Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2017

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2017

Galamukani! ndi magazini imene imafalitsidwa kwambiri padziko lonse.

Magazini oposa 360 miliyoni amasindikizidwa m’zilankhulo zoposa 100

ANTHU AKALE

ANTHU NDI MAYIKO

CHIPEMBEDZO

 • Kodi Baibulo Ndi Lochokeradi Kwa Mulungu? Na. 3

KUCHEZA NDI ANTHU

 • Katswiri Woona za Ubongo Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake (Rajesh Kalaria): Na. 4

 • Katswiri Wopanga Mapulogalamu a Pakompyuta Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake (Dr. Fan Yu): Na. 3

KUCHITA ZINTHU NDI ANTHU

 • Ana Akakula N’kuchoka Pakhomo (banja): Na. 4

 • Kodi Kuphunzitsa Ana Ntchito Zapakhomo N’kothandiza Bwanji? (kulera ana): Na. 3

 • Kodi Mumakonda Masewera Oika Moyo Pangozi? (achinyamata): Na. 5

 • Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Mumayamikira Zimene Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Amachita? (banja): Na. 1

 • Kumwetulira Ndi Mphatso Yofunika Kugawana: Na. 1

 • ‘Kusankha Dzina Labwino Ndi Kwabwino Kusiyana ndi Chuma Chochuluka’: Na. 4

 • Mungaphunzitse Bwanji Ana Anu Kukhala Odzichepetsa? (kulera ana): Na. 6

 • Mungatani Ngati Muli ndi Chisoni Chifukwa cha Imfa ya Bambo Kapena Mayi Anu? (achinyamata): Na. 2

 • Zimene Zimachitika Ana Akakhala ndi Chisoni: Na. 2

MBONI ZA YEHOVA

 • “Chikondi Chimene Anatisonyeza Chinatikhudza Kwambiri”(chivomerezi ku Nepal): Na. 1

NYAMA NDI ZOMERA

 • Mbalame ya Kunyanja Yochititsa Chidwi Kwambiri: Na. 4

SAYANSI

 • Mitsempha Imene Imagwira Ntchito Ngati Ubongo: Na. 3

 • Njuchi Zimatera Mochititsa Chidwi: Na. 2

 • Nyerere Yokhala Ndi Zinthu Zoiteteza ku Dzuwa: Na. 1

 • Tizipatso Tokongola Kwambiri ta Buluu: Na. 4

 • Ubweya wa Katumbu: Na. 3

 • Zigoba za Nkhono Zam’madzi: Na. 5

UMOYO NDI MANKHWALA

 • N’chifukwa Chiyani Achinyamata Ambiri Akudwala Matenda Ovutika Maganizo? Na. 1

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

ZOCHITIKA PADZIKO

 • Kodi Zinthu Padzikoli Zafika Poipa Kwambiri?

  Na. 6

 • Zimene Tingachite Kuti Tipulumuke Pakachitika Ngozi Zadzidzidzi: Na. 5

ZOSIYANASIYANA

 • Kodi Inuyo Mumatanganidwa Kwambiri? Na. 4

 • Kodi Ndi Bwino Kukhulupirira Zamatsenga? Na. 2

 • Magetsi Ndi Mafuta: Na. 5