BAIBO YA DZIKO LATSOPANO

2 Petulo—Za m’Bukuli

Cinyanja
2 Petulo—Za m’Bukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt 2 Petro

Kalata Yaciwili ya Petulo

Macaputala

1 2 3

Za m'Bukuli

  • 1

    • Moni (1)

    • Cititsani kuitanidwa kwanu kukhala kotsimikizika (2-15)

      • Makhalidwe ofunika kuonjezela pa cikhulupililo (5-9)

    • Mau aulosi ndi odalilika kwambili (16-21)

  • 2

    • Aphunzitsi abodza adzaonekela (1-3)

    • Aphunzitsi onyenga sadzalephela kuweluzidwa (4-10a)

      • Angelo anaponyedwa mu Tatarasi (4)

      • Cigumula; Sodomu ndi Gomora (5-7)

    • Mmene tingadziwile aphunzitsi onyenga (10b-22)

  • 3

    • Anthu onyoza amakaikila za cionongeko cimene cikubwela (1-7)

    • Yehova sakucedwa (8-10)

    • Ganizilani za mtundu wa anthu amene muyenela kukhala (11-16)

      • Kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano (13)

    • Cenjelani kuti anthu asakusoceletseni (17, 18)