Uthenga Wabwino Wolembedwa ndi Luka
Macaputala
Za m'Bukuli
-
-
Kalata yopita kwa Teofilo (1-4)
-
Mngelo Gabirieli anenelatu za kubadwa kwa Yohane M’batizi (5-25)
-
Mngelo Gabirieli anenelatu za kubadwa kwa Yesu (26-38)
-
Mariya apita kwa Elizabeti (39-45)
-
Mariya alemekeza Yehova (46-56)
-
Kubadwa kwa Yohane ndi mmene anamupatsila dzina (57-66)
-
Ulosi wa Zekariya (67-80)
-
-
-
Yesu ndiye “Mbuye wa Sabata” (1-5)
-
Munthu wopuwala dzanja acilitsidwa (6-11)
-
Atumwi 12 (12-16)
-
Yesu aphunzitsa ndi kucilitsa (17-19)
-
Anthu acimwemwe komanso anthu atsoka (20-26)
-
Kukonda adani (27-36)
-
Lekani kuweluza ena (37-42)
-
Umadziwika ndi zipatso zake (43-45)
-
Nyumba yomangidwa bwino; nyumba yopanda maziko (46-49)
-
-
-
Azimai amene anali kutsatila Yesu (1-3)
-
Fanizo la wofesa mbeu (4-8)
-
Cifukwa cake Yesu anagwilitsa nchito mafanizo (9, 10)
-
Afotokoza tanthauzo la fanizo la wofesa mbeu (11-15)
-
Nyale saibwinikila (16-18)
-
Amai ake a Yesu ndi abale ake (19-21)
-
Yesu aleketsa namondwe (22-25)
-
Yesu atumiza ziwanda m’nkhumba (26-39)
-
Mwana wamkazi wa Yairo; mzimai agwila cobvala cakunja ca Yesu (40-56)
-
-
-
Alangiza atumwi 12 molalikilila (1-6)
-
Herode adabwa naye kwambili Yesu (7-9)
-
Yesu adyetsa anthu 5,000 (10-17)
-
Petulo azindikila kuti Yesu ndi Khristu (18-20)
-
Yesu anenelatu za imfa yake (21, 22)
-
Zimene ophunzila oona a Yesu amacita (23-27)
-
Kusandulika kwa Yesu (28-36)
-
Kamnyamata kogwidwa ndi ciwanda kacilitsidwa (37-43a)
-
Kaciwili, Yesu anenelatu za imfa yake (43b-45)
-
Ophunzila akangana zakuti wamkulu ndani (46-48)
-
Aliyense amene satsutsana nafe ali ku mbali yathu (49, 50)
-
Mudzi wina wa Asamariya ukana Yesu (51-56)
-
Mmene tingatsatilile Yesu (57-62)
-
-
-
Zofufumitsa za Afarisi (1-3)
-
Opani Mulungu, osati anthu (4-7)
-
Kubvomeleza kuti ndife ophunzila a Khristu (8-12)
-
Fanizo la munthu wacuma wopusa (13-21)
-
Lekani kuda nkhawa (22-34)
-
Kagulu ka nkhosa (32)
-
-
Kukhala maso (35-40)
-
Woyang’anila wokhulupilika komanso woyang’anila wosakhulupilika (41-48)
-
Osati mtendele, koma magawano (49-53)
-
Kufunika kodziwa tanthauzo la zimene zikucitika (54-56)
-
Kuthetsa mikangano (57-59)
-
-
-
Lapani, apo ai muonongedwa (1-5)
-
Fanizo la mtengo wamkuyu wosabala zipatso (6-9)
-
Mzimai wopindika msana acilitsidwa pa Sabata (10-17)
-
Fanizo la kanjele ka mpilu komanso la zofufumitsa (18-21)
-
Khama n’lofunika kuti tilowe pa khomo lopanikiza (22-30)
-
Herode achulidwa kuti “nkhandwe” (31-33)
-
Yesu adandaula za Yerusalemu (34, 35)
-
-
-
Ansembe akonza ciwembu ca kupha Yesu (1-6)
-
Kukonzekela Pasika wothela (7-13)
-
Kukhazikitsidwa kwa Mgonelo wa Ambuye (14-20)
-
“Wondipeleka uja ali nane pathebulo pano” (21-23)
-
Akangana kwambili zakuti wamkulu ndani (24-27)
-
Cipangano ca Yesu ca Ufumu (28-30)
-
Yesu akambilatu zakuti Petulo adzamukana (31-34)
-
Kufunika kokhala okonzeka; malupanga awili (35-38)
-
Pemphelo la Yesu pa Phili la Maolivi (39-46)
-
Yesu agwidwa (47-53)
-
Petulo akana Yesu (54-62)
-
Yesu acitidwa zacipongwe (63-65)
-
Azengedwa mlandu ku Khoti Yaikulu ya Ayuda (66-71)
-

