BAIBO YA DZIKO LATSOPANO

2 Timoteyo—Za m’Bukuli

Cinyanja
2 Timoteyo—Za m’Bukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt 2 Timoteo

Kalata Yaciwili kwa Timoteyo

Macaputala

1 2 3 4

Za m'Bukuli

  • 1

    • Mau oyamba (1, 2)

    • Paulo ayamika Mulungu cifukwa ca cikhulupililo ca Timoteyo (3-5)

    • Kukolezela mphatso ya Mulungu ngati moto (6-11)

    • Kugwilitsitsa mau olondola (12-14)

    • Adani komanso mabwenzi a Paulo (15-18)

  • 2

    • Kuphunzitsa oyenelela kukhala aphunzitsi (1-7)

    • Kupilila mabvuto cifukwa ca uthenga wabwino (8-13)

    • Kufotokoza bwino mau a uthenga wabwino (14-19)

    • Kuthawa zilakolako za unyamata (20-22)

    • Mocitila ndi otsutsa (23-26)

  • 3

    • Masiku otsiliza adzakhala nthawi yobvuta (1-7)

    • Kutengela citsanzo ca Paulo mosamala (8-13)

    • “Pitiliza kutsatila zimene unaphunzila” (14-17)

      • Malemba onse anauzilidwa ndi Mulungu (16)

  • 4

    • “Uzikwanilitsa mbali zonse za utumiki wako” (1-5)

      • Lalikila mau modzipeleka (2)

    • “Ndamenya nkhondo yabwino” (6-8)

    • Zina zimene Paulo anakamba (9-18)

    • Kupeleka moni (19-22)